Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 118:22 - Buku Lopatulika

22 Mwala umene omangawo anaukana wakhala mutu wa pangodya.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Mwala umene omangawo anaukana wakhala mutu wa pangodya.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 Mwala umene amisiri omanga nyumba adaukana, womwewo wasanduka mwala wapangodya.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 Mwala umene amisiri omanga nyumba anawukana wasanduka wapangodya;

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 118:22
8 Mawu Ofanana  

chifukwa chake Ambuye Yehova atero, Taonani, ndiika mu Ziyoni mwala wa maziko, mwala woyesedwa mwala wa pangodya, wa mtengo wake wokhazikika ndithu; wokhulupirira sadzafulumira.


Ndiwe yani, phiri lalikulu iwe? Pamaso pa Zerubabele udzasanduka chidikha; ndipo adzatulutsa mwala woikidwa pamwamba, ndi kufuula, Chisomo, chisomo nao.


Yesu ananena kwa iwo, Kodi simunawerenge konse m'malembo, Mwala umene anaukana omanga nyumba womwewu unakhala mutu wa pangodya: Ichi chinachokera kwa Ambuye, ndipo chili chozizwitsa m'maso mwathu?


Koma Iye anawapenyetsa iwo, nati, Nchiyani ichi chinalembedwa, Mwala umene anaukana omanga nyumba, womwewu unakhala mutu wa pangodya.


Iye ndiye mwalawo woyesedwa wopanda pake ndi inu omanga nyumba, umene unayesedwa mutu wa pangodya.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa