Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 118:21 - Buku Lopatulika

21 Ndidzakuyamikani, popeza munandiyankha, ndipo munakhala chipulumutso changa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 Ndidzakuyamikani, popeza munandiyankha, ndipo munakhala chipulumutso changa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Ndikukuyamikani popeza kuti mwandiyankha, ndipo mwasanduka Mpulumutsi wanga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Ndidzakuyamikani chifukwa Inu munandiyankha; mwakhala chipulumutso changa.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 118:21
7 Mawu Ofanana  

Ndimkonda, popeza Yehova amamva mau anga ndi kupemba kwanga.


Yehova ndiye mphamvu yanga ndi nyimbo yanga; ndipo anakhala chipulumutso changa.


Yehova ndiye mphamvu yanga ndi nyimbo yanga, ndipo wakhala chipulumutso changa; ameneyo ndiye Mulungu wanga, ndidzamlemekeza; ndiye Mulungu wa kholo langa, ndidzamveketsa.


Taonani, Mulungu ndiye chipulumutso changa; ndidzakhulupirira, sindidzaopa; pakuti Yehova Mwini ndiye mphamvu yanga ndi nyimbo yanga, Iye ndiye chipulumutso changa.


Atero Yehova, Nthawi yondikomera ndakuyankha Iwe, ndi tsiku la chipulumutso ndakuthandiza; ndipo ndidzakusunga ndi kupatsa Iwe ukhale pangano la anthu, kuti ukhazikitse dziko, nuwalowetse m'zolowa zopasuka m'malo abwinja;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa