Masalimo 118:20 - Buku Lopatulika20 Chipata cha Yehova ndi ichi; olungama adzalowamo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Chipata cha Yehova ndi ichi; olungama adzalowamo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Ichi ndicho chipata cha Chauta, anthu okhawo ochita chifuniro chake adzaloŵera pamenepa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Ichi ndicho chipata cha Yehova chimene olungama mtima okha adzalowerapo. Onani mutuwo |