Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 118:19 - Buku Lopatulika

19 Nditsegulireni zipata za chilungamo; ndidzalowamo, ndidzayamika Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

19 Nditsegulireni zipata za chilungamo; ndidzalowamo, ndidzayamika Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

19 Tsekulireni zipata za Nyumba ya Mulungu, kuti ndifike ku malo ake achilungamo, ndikathokoze Chauta.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

19 Tsekulireni zipata zachilungamo, kuti ndifike kudzayamika Yehova.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 118:19
10 Mawu Ofanana  

Lowani kuzipata zake ndi chiyamiko, ndi kumabwalo ake ndi chilemekezo: Myamikeni; lilemekezeni dzina lake.


Mulungu, mokhala mwake moyera, ndiye Atate wa ana amasiye, ndi woweruza wa akazi amasiye.


Tidze nacho chiyamiko pamaso pake, timfuulire Iye mokondwera ndi nyimbo.


Tsegulani pazipata, kuti mtundu wolungama, umene uchita zoonadi, ulowemo.


Yehova ndiye wondipulumutsa ine; Chifukwa chake tidzaimba nyimbo zanga, ndi zoimba zazingwe Masiku onse a moyo wathu m'nyumba ya Yehova.


Hezekiya anatinso, Chizindikiro nchiyani, kuti ndidzakwera kunka kunyumba ya Yehova?


Odala iwo amene atsuka miinjiro yao, kuti akakhale nao ulamuliro pa mtengo wa moyo, ndi kuti akalowe m'mzinda pazipata.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa