Masalimo 118:18 - Buku Lopatulika18 Kulanga anandilangadi Yehova: koma sanandipereke kuimfa ai. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Kulanga anandilangadi Yehova: koma sanandipereke kuimfa ai. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Chauta wandilanga koopsa, koma sadandisiye kuti ndife. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Yehova wandilanga koopsa, koma sanandipereke ku imfa. Onani mutuwo |