Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 118:17 - Buku Lopatulika

17 Sindidzafa koma ndidzakhala ndi moyo, ndipo ndidzafotokozera ntchito za Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Sindidzafa koma ndidzakhala ndi moyo, ndipo ndidzafotokozera ntchito za Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Sindidzafa, ndidzakhala moyo, ndipo ndidzalalika ntchito za Chauta.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Sindidzafa koma ndidzakhala ndi moyo ndipo ndidzalalika za ntchito ya Yehova.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 118:17
13 Mawu Ofanana  

Ndipo apereke nsembe zachiyamiko, nafotokozere ntchito zake ndi kufuula mokondwera.


Ndinafotokozera ndi milomo yanga maweruzo onse a pakamwa panu.


Mbadwo wina udzalemekezera ntchito zanu mbadwo unzake, ndipo udzalalikira zamphamvu zanu.


Chilungamo chanu sindinachibise m'kati mwamtima mwanga; chikhulupiriko chanu ndi chipulumutso chanu ndinachinena; chifundo chanu ndi choonadi chanu sindinachibisire msonkhano waukulu.


Inu, Yehova, Mulungu wanga, zodabwitsa zanu mudazichita nzambiri, ndipo zolingirira zanu za pa ife; palibe wina wozifotokozera Inu; ndikazisimba ndi kuzitchula, zindichulukira kuziwerenga.


Pakuti muimfa m'mosakumbukira Inu; m'mandamo adzakuyamikani ndani?


Koma ine, kundikomera kuyandikiza kwa Mulungu. Ndimuyesa Ambuye Yehova pothawirapo ine, kuti ndifotokozere ntchito zanu zonse.


Yehova watulutsa chilungamo chathu; tiyeni tilalikire mu Ziyoni ntchito ya Yehova Mulungu wathu.


Si ndinu wachikhalire, Yehova Mulungu wanga, wopatulika wanga? Sitidzafa. Yehova munamuikiratu kuti aweruzidwe; ndipo Inu, Thanthwe, munamkhazika kuti alangidwe.


Koma Yesu pamene anamva, anati, Kudwala kumene sikuli kwa imfa, koma chifukwa cha ulemerero wa Mulungu, kuti Mwana wa Mulungu alemekezedwe nako.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa