Masalimo 118:16 - Buku Lopatulika16 Dzanja lamanja la Yehova likwezeka, Dzanja lamanja la Yehova lichita mwamphamvu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Dzanja lamanja la Yehova likwezeka, Dzanja lamanja la Yehova lichita mwamphamvu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 dzanja lamanja la Chauta lapambana, dzanja lamanja la Chauta limagonjetsa mwamphamvu.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Dzanja lamanja la Yehova latukulidwa mmwamba Dzanja lamanja la Yehova lachita zamphamvu!” Onani mutuwo |