Masalimo 118:23 - Buku Lopatulika23 Ichi chidzera kwa Yehova; nchodabwitsa ichi pamaso pathu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Ichi chidzera kwa Yehova; nchodabwitsa ichi pamaso pathu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Chauta ndiye amene wachita zimenezi, zimenezi nzodabwitsa pamaso pathu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Yehova ndiye wachita zimenezi ndipo nʼzodabwitsa pamaso pathu. Onani mutuwo |