Masalimo 115:9 - Buku Lopatulika9 Israele, khulupirira Yehova: Ndiye mthandizi wao ndi chikopa chao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Israele, khulupirira Yehova: Ndiye mthandizi wao ndi chikopa chao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Iwe Israele, khulupirira Chauta. Chauta ndiye mthandizi wako ndi chishango chako. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Inu Aisraeli, dalirani Yehova; Iye ndiye thandizo lanu ndi chishango chanu. Onani mutuwo |