Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 115:8 - Buku Lopatulika

8 Adzafanana nao iwo akuwapanga; ndi onse akuwakhulupirira.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

8 Adzafanana nao iwo akuwapanga; ndi onse akuwakhulupirira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

8 Anthu amene amapanga mafanowo amafanafana nawo, chimodzimodzi onse amene amaŵakhulupirira.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

8 Anthu amene amapanga mafanowo adzafanana nawo, chimodzimodzinso onse amene amadalira mafanowo.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 115:8
6 Mawu Ofanana  

Akuwapanga adzafanana nao; inde, onse akuwakhulupirira.


Anthu onse ali opulukira ndi opanda nzeru; woyenga yense anyazitsidwa ndi fanizo lake losemasema; pakuti fanizo lake loyenga lili bodza, mulibe mpweya mwa iwo.


Koma onse pamodzi apulukira ndi kupusa; mtengo ndiwo chilangizo, chopanda pake.


Iwo osamalira mabodza opanda pake ataya chifundo chaochao.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa