Masalimo 115:7 - Buku Lopatulika7 manja ali nao, koma osagwira; mapazi ali nao, koma osayenda; kapena sanena pammero pao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 manja ali nao, koma osagwira; mapazi ali nao, koma osayenda; kapena sanena pammero pao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Manja ali nawo, koma akakhudza, samva kanthu. Miyendo ali nayo, koma sayenda, ndipo satulutsa ndi liwu lomwe kukhosi kwao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 manja ali nawo koma akakhudza samva kanthu; mapazi ali nawo koma sayenda; kapena pakhosi pawo kutulutsa mawu. Onani mutuwo |