Masalimo 115:6 - Buku Lopatulika6 makutu ali nao, koma osamva; mphuno ali nazo, koma osanunkhiza; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 makutu ali nao, koma osamva; mphuno ali nazo, koma osanunkhiza; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Makutu ali nawo, koma saamva. Mphuno ali nazo, koma sanunkhiza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 makutu ali nawo koma samva, mphuno ali nazo koma sanunkhiza; Onani mutuwo |