Masalimo 115:5 - Buku Lopatulika5 Pakamwa ali napo, koma osalankhula; maso ali nao, koma osapenya; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Pakamwa ali napo, koma osalankhula; maso ali nao, koma osapenya; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Pakamwa ali napo, koma salankhula. Maso ali nawo, koma sapenya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Pakamwa ali napo koma sayankhula, maso ali nawo koma sapenya; Onani mutuwo |