Masalimo 112:9 - Buku Lopatulika9 Anagawagawa, anapatsa aumphawi; chilungamo chake chikhalitsa kosatha; nyanga yake idzakwezeka ndi ulemu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Anagawagawa, anapatsa aumphawi; chilungamo chake chikhalitsa kosatha; nyanga yake idzakwezeka ndi ulemu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Amapereka chithandizo mwaufulu, amaoloŵa manja kwa anthu osauka. Chilungamo chake chidzakhala chamuyaya, adzakhala wamphamvu ndipo anthu adzampatsa ulemu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Wopereka mphatso zake mowolowamanja kwa osauka, chilungamo chake chimanka mpaka muyaya; nyanga yake idzakwezedwa mwaulemu. Onani mutuwo |