Masalimo 112:7 - Buku Lopatulika7 Sadzaopa mbiri yoipa; mtima wake ngwokhazikika, wokhulupirira Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Sadzaopa mbiri yoipa; mtima wake ngwokhazika, wokhulupirira Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Saopa akamva zoipa zimene zachitika. Mtima wake ndi wosasinthika, amakhulupirira Chauta. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Saopa akamva zoyipa zimene zachitika; mtima wake ndi wokhazikika ndipo amadalira Yehova. Onani mutuwo |