Masalimo 112:6 - Buku Lopatulika6 Popeza sadzagwedezeka nthawi zonse; wolungama adzakumbukika ku nthawi yosatha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Popeza sadzagwedezeka nthawi zonse; wolungama adzakumbukika ku nthawi yosatha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Pakuti munthu wochita chilungamo sadzagwedezeka konse, sadzaiŵalika mpaka muyaya. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Ndithu sadzagwedezeka; munthu wolungama sadzayiwalika mpaka muyaya. Onani mutuwo |