Masalimo 112:4 - Buku Lopatulika4 Kuunika kutulukira oongoka mtima mumdima; Iye ndiye wachisomo, ndi wansoni ndi wolungama. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Kuunika kutulukira oongoka mtima mumdima; Iye ndiye wachisomo, ndi wansoni ndi wolungama. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Ngakhale nthaŵi ya mdima, munthu wochita chilungamo ayenda m'kuŵala, chifukwa ngwokoma mtima, wachifundo ndi woongoka. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ngakhale mu mdima kuwala kumatulukira olungama mtima; wokoma mtima, wachifundo ndi wowongoka mtima. Onani mutuwo |