Masalimo 110:5 - Buku Lopatulika5 Ambuye padzanja lamanja lako adzaphwanya mafumu tsiku la mkwiyo wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Yehova pa dzanja lamanja lako adzaphwanya mafumu tsiku la mkwiyo wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Ambuye ali pambali pako. Adzaphwanya mafumu pa tsiku la mkwiyo wao. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Ambuye ali kudzanja lako lamanja; Iye adzaponda mafumu pa tsiku la ukali wake. Onani mutuwo |