Masalimo 110:1 - Buku Lopatulika1 Yehova ananena kwa Ambuye wanga, Khalani padzanja lamanja langa, kufikira nditaika adani anu chopondapo mapazi anu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Yehova ananena kwa Ambuye wanga, Khalani pa dzanja lamanja langa, kufikira nditaika adani anu chopondapo mapazi anu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Chauta adauza Mbuye wanga kuti, “Khala ku dzanja langa lamanja, mpaka nditasandutsa adani ako kukhala ngati chopondapo mapazi ako.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Yehova akuwuza Mbuye wanga kuti, “Khala ku dzanja langa lamanja mpaka nditasandutsa adani ako kukhala chopondapo mapazi ako.” Onani mutuwo |