Masalimo 11:2 - Buku Lopatulika2 Pakuti, onani, oipa akoka uta, apiringidza muvi wao pansinga, kuwaponyera mumdima oongoka mtima. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Pakuti, onani, oipa akoka uta, apiringidza muvi wao pansinga, kuwaponyera mumdima oongoka mtima. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Taonani, anthu oipa akunga uta ndipo akwinja muvi pa nsinga, kuti alase anthu a mtima wolungama. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Pakuti taona oyipa akunga mauta awo; ayika bwino mivi yawo pa zingwe za uta, pobisala pawo kuti alase olungama mtima. Onani mutuwo |