Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 11:3 - Buku Lopatulika

3 Akapasuka maziko, wolungama angachitenji?

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Akapasuka maziko, wolungama angachitenji?

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 Tsono ngati maziko aonongeka, nanga wolungama angachite chiyani?”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Tsono ngati maziko awonongeka, olungama angachite chiyani?”

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 11:3
15 Mawu Ofanana  

Koma wolungama asungitsa njira yake, ndi iye wa manja oyera adzakulabe mumphamvu.


Lasungunuka dziko lapansi, ndi onse okhalamo; ndinachirika mizati yake.


Sadziwa, ndipo sazindikira; amayendayenda mumdima; maziko onse a dziko lapansi agwedezeka.


Ndipo iwo amene adzakhala a iwe adzamanga malo akale abwinja; udzautsa maziko a mibadwo yambiri; udzatchedwa Wokonza pogumuka, Wakubwezera njira zakukhalamo.


Koma ndithu maziko a Mulungu aimika pokhazikika, ndi kukhala nacho chizindikiro ichi, Ambuye azindikira iwo amene ali ake; ndipo, Adzipatule kwa chosalungama yense wakutchula dzina la Ambuye.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa