Masalimo 11:1 - Buku Lopatulika1 Ndakhulupirira Yehova, mutani nkunena kwa moyo wanga, Thawirani kuphiri lanu ngati mbalame? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ndakhulupirira Yehova, mutani nkunena kwa moyo wanga, Thawirani kuphiri lanu ngati mbalame? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Ndimathaŵira kwa Chauta. Nanga mungathe bwanji kundiwuza kuti, “Thaŵira ku mapiri ngati mbalame. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Mwa Yehova ine ndimathawiramo. Nanga mungathe bwanji kunena kwa ine kuti, “Thawira ku phiri lako ngati mbalame. Onani mutuwo |