Masalimo 108:9 - Buku Lopatulika9 Mowabu ndiye mkhate wanga; pa Edomu ndidzaponya nsapato yanga; ndidzafuulira Filistiya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Mowabu ndiye mkhate wanga; pa Edomu ndidzaponya nsapato yanga; ndidzafuulira Filistiya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 “Mowabu adzakhala ngati mbale yosambiramo ine. Edomu adzakhala poponda nsapato zanga. Ndidzafuula mokondwa nditagonjetsa Filistiya.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Mowabu ndi mbale yanga yosambiramo ndidzaponya nsapato zanga pa Edomu; ndidzafuwula mopambana pa Filisitiya.” Onani mutuwo |