Masalimo 108:10 - Buku Lopatulika10 Adzandifikitsa ndani m'mzinda wa m'linga? Adzanditsogolera ndani ku Edomu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Adzandifikitsa ndani m'mudzi wa m'linga? Adzanditsogolera ndani ku Edomu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Ndani adzandifikitse ku mzinda wamalinga? Ndani adzanditsogolere ku Edomu? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Ndani adzandifikitsa ku mzinda wotetezedwa? Ndani adzanditsogolera ku Edomu? Onani mutuwo |