Masalimo 108:11 - Buku Lopatulika11 Si ndinu Mulungu, amene mwatitaya osatuluka nao magulu athu? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Si ndinu Mulungu, amene mwatitaya osatuluka nao magulu athu? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Si wina ai koma ndinu Mulungu amene mwatitaya, ndinu Mulungu amene mwaleka kuperekeza ankhondo athu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Kodi sindinu Mulungu, Inu amene mwatikana ndipo simuperekezanso magulu athu ankhondo? Onani mutuwo |