Masalimo 108:8 - Buku Lopatulika8 Giliyadi ndi wanga, Manase ndi wanga; ndi Efuremu ndiye mphamvu ya mutu wanga; Yuda ndiye wolamulira wanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Giliyadi ndi wanga, Manase ndi wanga; ndi Efuremu ndiye mphamvu ya mutu wanga; Yuda ndiye wolamulira wanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 “Giliyadi ndi wanga, Manase ndi wanga. Efuremu ali ngati chisoti changa chodzitetezera. Yuda ali ngati ndodo yanga yaufumu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Giliyadi ndi wanga, Manase ndi wanganso; Efereimu ndi chipewa changa chodzitetezera, Yuda ndi ndodo yanga yaufumu. Onani mutuwo |