Masalimo 108:7 - Buku Lopatulika7 Mulungu analankhula m'chiyero chake; ndidzakondwerera: ndidzagawa Sekemu; ndidzayesa muyeso chigwa cha Sukoti. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Mulungu analankhula m'chiyero chake; ndidzakondwerera: ndidzagawa Sekemu; ndidzayesa muyeso chigwa cha Sukoti. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Mulungu ali ku malo ake oyera, walonjeza kuti, “Ndidzakugaŵirani dziko la Sekemu mokondwa, ndidzakulemberani malire m'chigwa cha Sukoti. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Mulungu wayankhula kuchokera ku malo ake opatulika: “Mwachipambano Ine ndidzagawa Sekemu ndipo ndidzayesa chigwa cha Sukoti. Onani mutuwo |