Masalimo 108:5 - Buku Lopatulika5 Kwezekani pamwamba pa thambo, Mulungu; ndi ulemerero wanu pamwamba padziko lonse lapansi, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Kwezekani pamwamba pa thambo, Mulungu; ndi ulemerero wanu pamwamba pa dziko lonse lapansi, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Inu Mulungu, onetsani ukulu wanu mumlengalenga monse. Wanditsani ulemerero wanu pa dziko lonse lapansi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Kwezekani Inu Mulungu, kuposa mayiko akumwamba, ndipo ulemerero wanu uphimbe dziko lonse lapansi. Onani mutuwo |