Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 108:4 - Buku Lopatulika

4 Pakuti chifundo chanu nchachikulu kupitirira kumwamba, ndi choonadi chanu kufikira mitambo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Pakuti chifundo chanu nchachikulu kupitirira kumwamba, ndi choonadi chanu kufikira mitambo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 pakuti chikondi chanu chosasinthika nchachikulu, chofika mpaka pamwamba pa mlengalenga, kukhulupirika kwanu kumafika mpaka ku mitambo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Pakuti chikondi chanu nʼchachikulu, kutalika kwake kuposa kumwamba; kukhulupirika kwanu kumafika mlengalenga.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 108:4
10 Mawu Ofanana  

Chifukwa chake ndidzakuongani Yehova, pakati pa amitundu, ndipo ndidzaimba zolemekeza dzina lanu.


Pakuti monga m'mwamba mutalikira ndi dziko lapansi, motero chifundo chake chikulira iwo akumuopa Iye.


Yehova akwezeka pamwamba pa amitundu onse, ulemerero wake pamwambamwamba.


Yehova, m'mwamba muli chifundo chanu; choonadi chanu chifikira kuthambo.


Chifundo ndi choonadi zakomanizana; chilungamo ndi mtendere zapsompsonana.


Pakuti ndinati, Chifundo adzachimanga kosaleka; mudzakhazika chikhulupiriko chanu mu Mwamba mwenimweni.


Ndipo kumwamba kudzalemekeza zodabwitsa zanu, Yehova; chikhulupiriko chanunso mu msonkhano wa oyera mtima.


Pakuti monga kumwamba kuli kutali ndi dziko lapansi, momwemo njira zanga zili zazitali kupambana njira zanu, ndi maganizo anga kupambana maganizo anu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa