Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 108:2 - Buku Lopatulika

2 Galamukani, chisakasa ndi zeze; ndidzauka ndekha mamawa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

2 Galamukani, chisakasa ndi zeze; ndidzauka ndekha mamawa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

2 Inu zeze ndi pangwe, tiyeni lirani. Ndidzadzutsa dzuŵa ndi nyimbo zanga.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

2 Dzukani, zeze ndi pangwe! Ine ndidzadzutsa mʼbandakucha.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 108:2
7 Mawu Ofanana  

Lemekezani Yehova, inu, ntchito zake zonse, ponseponse pali ufumu wake: Lemekeza Yehova, moyo wanga iwe.


Yamikani Yehova ndi zeze; muimbireni ndi chisakasa cha zingwe khumi.


Galamuka, ulemu wanga; galamukani chisakasa ndi zeze! Ndidzauka ndekha mamawa.


Ndidzalemekeza dzina la Mulungu ndi kuliimbira, ndipo ndidzambukitsa ndi kumyamika.


Utsani salimo, bwera nakoni kalingaka, zeze wokondwetsa pamodzi ndi chisakasa.


Galamuka, Debora, galamuka, galamuka, galamuka, unene nyimbo; uka, Baraki, manga nsinga ndende zako, mwana wa Abinowamu, iwe.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa