Masalimo 108:12 - Buku Lopatulika12 Tithandizeni mumsauko; pakuti chipulumutso cha munthu ndi chabe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Tithandizeni mumsauko; pakuti chipulumutso cha munthu ndi chabe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Tithandizeni kulimbana ndi adani athuwo, pakuti chithandizo cha munthu nchopandapake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Tithandizeni ife kulimbana ndi mdani, pakuti thandizo la munthu ndi lopanda pake. Onani mutuwo |