Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 102:9 - Buku Lopatulika

9 Pakuti ndadya mapulusa ngati mkate, ndi kusakaniza chomwera changa ndi misozi,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Pakuti ndadya mapulusa ngati mkate, ndi kusanganiza chomwera changa ndi misozi,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Inetu ndimadya phulusa ngati chakudya, chakumwa changa ndimasakaniza ndi misozi,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Pakuti ndimadya phulusa ngati chakudya changa ndi kusakaniza chakumwa changa ndi misozi

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 102:9
10 Mawu Ofanana  

Pakuti ndikati ndidye, kumadza kuusa moyo kwanga; ndi kudzuma kwanga kumathiridwa ngati madzi.


Udziweramiranji moyo wanga iwe? Ndi kuzingwa m'kati mwanga? Yembekeza Mulungu; pakuti ndidzamlemekeza tsopanonso, ndiye chipulumutso cha nkhope yanga ndi Mulungu wanga.


Misozi yanga yakhala ngati chakudya changa, usana ndi usiku; pakunena iwo kwa ine dzuwa lonse, Mulungu wako ali kuti?


Ndipo anandipatsa ndulu ikhale chakudya changa; nandimwetsa vinyo wosasa pomva ludzu ine.


Munawadyetsa mkate wa misozi, ndipo munawamwetsa misozi yambiri.


Iye adya phulusa; mtima wodzinyenga wampambutsa, kuti iye sangapulumutse moyo wake, pena kunena, Kodi simuli kunama m'dzanja langa lamanja?


Musachifotokoza mu Gati, musalira misozi konse; m'nyumba ya Afira ndinagubuduka m'fumbi.


Adzanyambita fumbi ngati njoka; ngati zokwawa za padziko, adzanjenjemera potuluka m'ngaka mwao; adzafika kwa Yehova Mulungu wao ndi mantha, nadzaopa chifukwa cha iwe.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa