Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 102:10 - Buku Lopatulika

10 chifukwa cha ukali wanu ndi kuzaza kwanu; popeza munandinyamula ndipo munandigwetsa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 chifukwa cha ukali wanu ndi kuzaza kwanu; popeza munandinyamula ndipo munandigwetsa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 chifukwa cha ukali wanu ndi mkwiyo wanu, popeza kuti Inu mwandinyamula ndi kunditaya.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 chifukwa cha ukali wanu waukulu, popeza Inu mwandinyamula ndi kunditayira kumbali.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 102:10
16 Mawu Ofanana  

Koma ngati mumuka, chitani, limbikani kunkhondo, Mulungu adzakugwetsani pamaso pa adani; pakuti Mulungu ali nayo mphamvu yakuthandiza ndi yakugwetsa.


Yehova agwiriziza ofatsa; atsitsira oipa pansi.


Pakuti ndidzafotokozera mphulupulu yanga; nditenga nkhawa chifukwa cha tchimo langa.


Mumnofu mwanga mulibe chamoyo chifukwa cha ukali wanu; ndipo m'mafupa anga simuzizira, chifukwa cha cholakwa changa.


Pamene mulanga munthu ndi zomdzudzula chifukwa cha mphulupulu, mukanganula kukongola kwake monga mumachita ndi njenjete. Indedi, munthu aliyense ali chabe.


Ndidzikumbukira izi ndipo nditsanulira moyo wanga m'kati mwa ine, pakuti ndinkapita ndi unyinji wa anthu, ndinawatsogolera kunyumba ya Mulungu, ndi mau akuimbitsa ndi kuyamika, ndi unyinji wakusunga dzuwa lokondwera.


Yehova ali wolungama; pakuti ndapikisana ndi m'kamwa mwake; mumvetu, mitundu ya anthu nonsenu, nimuone chisoni changa; anamwali ndi anyamata anga atha kulowa m'ndende.


Korona wagwa pamutu pathu; kalanga ife! Pakuti tinachimwa.


Ndipo tidziwa kuti zinthu zilizonse chizinena chilamulo chizilankhulira iwo ali nacho chilamulo; kuti pakamwa ponse patsekedwe, ndi dziko lonse lapansi litsutsidwe ndi Mulungu;


olondoleka, koma osatayika; ogwetsedwa, koma osaonongeka;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa