Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 102:7 - Buku Lopatulika

7 Ndidikira, ndikhala ngati mbalame ili yokha pamwamba pa tsindwi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

7 Ndidikira, ndikhala ngati mbalame ili yokha pamwamba pa tsindwi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

7 Ndimagona osapeza tulo, ndili ngati mbalame yokhala yokha pa denga,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

7 Ndimagona osapeza tulo; ndakhala ngati mbalame yokhala yokha pa denga.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 102:7
9 Mawu Ofanana  

Ndili mbale wao wa ankhandwe, ndi mnansi wao wa nthiwatiwa.


Moyo wanga uyang'anira Ambuye, koposa alonda matanda kucha; inde koposa alonda matanda kucha.


Mulungu wanga, ndiitana usana, koma simuvomereza; ndipo usiku, sindikhala chete.


Ondikonda ndi anzanga apewa mliri wanga; ndipo anansi anga aima patali.


Mundikhalitsa maso; ndigwidwa mtima wosanena kanthu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa