Masalimo 102:6 - Buku Lopatulika6 Ndikunga vuwo m'chipululu; ndikhala ngati kadzidzi wa kumabwinja. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndikunga vuwo m'chipululu; ndikhala ngati kadzidzi wa kumabwinja. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Ndili ngati mbalame yakuchipululu, ngati kadzidzi wam'mabwinja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Ndili ngati kadzidzi wa ku chipululu, monga kadzidzi pakati pa mabwinja. Onani mutuwo |