Masalimo 102:27 - Buku Lopatulika27 Koma Inu ndinu yemweyo, ndi zaka zanu sizifikira kutha. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Koma Inu ndinu yemweyo, ndi zaka zanu sizifikira kutha. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Koma Inu simusintha, zaka zanu sizitha. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Koma Inu simusintha, ndipo zaka zanu sizidzatha. Onani mutuwo |