Masalimo 102:25 - Buku Lopatulika25 Munakhazika dziko lapansi kalelo; ndipo zakumwamba ndizo ntchito ya manja anu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Munakhazika dziko lapansi kalelo; ndipo zakumwamba ndizo ntchito ya manja anu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Inu mudaika maziko a dziko lapansi kalekale, ndipo zakumwamba mudazipanga ndi manja anu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Pachiyambi Inu munakhazikitsa maziko a dziko lapansi ndipo mayiko akumwamba ndi ntchito ya manja anu. Onani mutuwo |