Masalimo 102:23 - Buku Lopatulika23 Iye analanda mphamvu yanga panjira; anachepsa masiku anga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Iye analanda mphamvu yanga panjira; anachepsa masiku anga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 Chauta wathyola mphamvu zanga ndisanakule, wafupikitsa masiku anga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 Iye anathyola mphamvu zanga pa nthawi ya moyo wanga; Iyeyo anafupikitsa masiku anga. Onani mutuwo |