Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 102:22 - Buku Lopatulika

22 Posonkhana pamodzi mitundu ya anthu, ndi maufumu kuti atumikire Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

22 Posonkhana pamodzi mitundu ya anthu, ndi maufumu kuti atumikire Yehova.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

22 pamene mitundu ya anthu ndi mafumu adzasonkhana kuti apembedze Chauta.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

22 pamene mitundu ya anthu ndi maufumu adzasonkhana kuti alambire Yehova.

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 102:22
11 Mawu Ofanana  

Ndodo yachifumu siidzachoka mwa Yuda, kapena wolamulira pakati pa mapazi ake, kufikira atadza Silo; ndipo anthu adzamvera iye.


Malekezero onse a dziko lapansi adzakumbukira nadzatembenukira kwa Yehova, ndipo mafuko onse a amitundu adzagwadira pamaso panu.


Mau a alonda ako! Akweza mau, aimba pamodzi; pakuti adzaona maso ndi maso, pamene Yehova abwerera kudza ku Ziyoni.


Kondwani zolimba, imbani pamodzi, inu malo abwinja a pa Yerusalemu; pakuti Yehova watonthoza mtima wa anthu ake, waombola Yerusalemu.


Ndipo Uthenga uwu Wabwino wa Ufumu udzalalikidwa padziko lonse lapansi, ukhale mboni kwa anthu a mitundu yonse; ndipo pomwepo chidzafika chimaliziro.


mu mphamvu ya zizindikiro ndi zozizwitsa, mu mphamvu ya Mzimu Woyera; kotero kuti ine kuyambira ku Yerusalemu ndi kuzungulirako kufikira ku Iliriko, ndinakwanitsa Uthenga Wabwino wa Khristu;


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa