Masalimo 102:21 - Buku Lopatulika21 Kuti anthu alalikire dzina la Yehova mu Ziyoni, ndi chilemekezo chake mu Yerusalemu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Kuti anthu alalikire dzina la Yehova m'Ziyoni, ndi chilemekezo chake m'Yerusalemu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Motero anthu adzalalika dzina la Chauta ku Ziyoni, ndipo adzamtamanda ku Yerusalemu, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Kotero dzina la Yehova lidzalengezedwa mu Ziyoni ndi matamando ake mu Yerusalemu, Onani mutuwo |