Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Masalimo 102:20 - Buku Lopatulika

20 kuti amve kubuula kwa wandende; namasule ana a imfa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

20 kuti amve kubuula kwa wandende; namasule ana a imfa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

20 kuti amve kubuula kwa anthu am'ndende, kuti aŵapulumutse amene adaayenera kuphedwa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

20 kuti amve kubuwula kwa anthu a mʼndende, kuti apulumutse amene anayenera kuphedwa.”

Onani mutuwo Koperani




Masalimo 102:20
15 Mawu Ofanana  

Koma Yehowahazi anapembedza Yehova, Yehova namvera; pakuti anapenya kupsinjika kwake kwa Israele m'mene mfumu ya Aramu inawapsinja.


M'mzinda waukulu anthu abuula alinkufa; ndi moyo wa iwo olasidwa ufuula; koma Mulungu sasamalira choipacho.


ndiye wakuchitira chiweruzo osautsika; ndiye wakupatsa anjala chakudya; Yehova amasula akaidi.


Kubuula kwa wandende kufike kuli Inu; monga mwa mphamvu yanu yaikulu lolani ana a imfa atsale.


Ndipo Yehova anati, Ndapenyetsetsa mazunzo a anthu anga ali mu Ejipito, ndamvanso kulira kwao chifukwa cha akuwafulumiza; pakuti ndidziwa zowawitsa zao;


amene anapululutsa dziko, napasula mizinda yake, amene sanamasule ndende zake, zinke kwao?


Penyani muli mokhalamo mwanu mopatulika, m'mwamba, ndipo dalitsani anthu anu Israele, ndi nthaka imene munatipatsa, monga munalumbirira makolo athu, dziko moyenda mkaka ndi uchi ngati madzi.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa