Masalimo 102:19 - Buku Lopatulika19 Pakuti anapenya pansi ali kumwamba kuli malo ake opatulika; Yehova pokhala kumwamba anapenya dziko lapansi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Pakuti anapenya pansi ali kumwamba kuli malo ake opatulika; Yehova pokhala kumwamba anapenya dziko lapansi; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Iye adayang'ana pansi ali m'malo ake oyera kumwamba, ali kumwambako, Chauta adayang'ana pa dziko lapansi, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 “Yehova anayangʼana pansi kuchokera ku malo ake opatulika mmwamba, kuchokera kumwamba anayangʼana dziko lapansi, Onani mutuwo |