Masalimo 102:16 - Buku Lopatulika16 Pakuti Yehova anamanga Ziyoni, anaoneka mu ulemerero wake; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Pakuti Yehova anamanga Ziyoni, anaoneka m'ulemerero wake; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Chauta adzamanganso Ziyoni, ndipo adzaonekera mu ulemerero wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Pakuti Yehova adzamanganso Ziyoni ndi kuonekera mu ulemerero wake. Onani mutuwo |