Hoseya 3:2 - Buku Lopatulika2 M'mwemo ndinadzigulira iye ndi masekeli khumi ndi asanu a siliva, ndi homeri ndi leteki wa barele; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 M'mwemo ndinadzigulira iye ndi masekeli khumi ndi asanu a siliva, ndi homeri ndi leteki wa barele; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Motero ndidamkwatira popereka ndalama khumi ndi zisanu zasiliva, ndiponso mitanga isanu ndi iŵiri ya barele. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Motero ndinamukwatira popereka ndalama khumi ndi zisanu zasiliva, ndiponso mitanga isanu ndi iwiri ya barele. Onani mutuwo |