Hoseya 3:3 - Buku Lopatulika3 ndipo ndinati kwa iye, Uzikhala ndi ine masiku ambiri, usachita chigololo, usakhala mkazi wa mwamuna aliyense; momwemo inenso nawe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 ndipo ndinati kwa iye, Uzikhala ndi ine masiku ambiri, usachita chigololo, usakhala mkazi wa mwamuna aliyense; momwemo inenso nawe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 Ndidamuuza mkaziyo kuti, “Uzikhala nane masiku ambiri, osachitanso zachiwerewere kapena chigololo ndi munthu wina. Nanenso ndidzachita chimodzimodzi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Kenaka ndinamuwuza mkaziyo kuti, “Ukhale nane masiku ambiri; usachitenso zachiwerewere kapena chigololo ndi munthu wina, ndipo ine ndidzakhala nawe.” Onani mutuwo |