Genesis 5:2 - Buku Lopatulika2 anawalenga iwo mwamuna ndi mkazi, nawadalitsa iwo natcha mtundu wao anthu, tsiku lomwe anawalenga iwo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 anawalenga iwo mwamuna ndi mkazi, nawadalitsa iwo natcha mtundu wao anthu, tsiku lomwe anawalenga iwo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Adalenga mwamuna ndi mkazi, ndipo adaŵadalitsa, naŵatchula dzina loti Anthu.) Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Iye analenga mwamuna ndi mkazi. Anawadalitsa ndipo anawatcha “Munthu.” Onani mutuwo |