Genesis 5:1 - Buku Lopatulika1 Ili ndi buku la mibadwo ya Adamu. Tsiku lomwe Mulungu analenga munthu anamlenga m'chifanizo cha Mulungu; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Ili ndi buku la mibadwo ya Adamu. Tsiku lomwe Mulungu analenga munthu anamlenga m'chifanizo cha Mulungu; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Mndandanda wa mibadwo yochokera mwa Adamu udayenda motere: (Mulungu polenga Adamu, adampanga muchifaniziro chake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Ndondomeko ya mibado ya Adamu ndi iyi: Pamene Mulungu analenga munthu, anamulenga mʼchifaniziro cha Mulungu. Onani mutuwo |