Genesis 4:26 - Buku Lopatulika26 Ndiponso kwa Seti, kwa iye kunabadwa mwana wamwamuna: anamutcha dzina lake Enosi: pomwepo anthu anayamba kutchula dzina la Yehova. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Ndiponso kwa Seti, kwa iye kunabadwa mwana wamwamuna: anamutcha dzina lake Enosi: pomwepo anthu anayamba kutchula dzina la Yehova. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Seti adabereka mwana namutcha Enosi. Nthaŵi imeneyo anthu adayamba kutama dzina la Chauta mopemba. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Seti naye anali ndi mwana wa mwamuna, ndipo anamutcha Enosi. Pa nthawi imeneyi anthu anayamba kupemphera mʼdzina la Yehova. Onani mutuwo |