Genesis 4:12 - Buku Lopatulika12 pamene udzalima panthaka siidzaperekanso kwa iwe mphamvu yake: udzakhala wothawathawa ndi woyendayenda padziko lapansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 pamene udzalima panthaka siidzaperekanso kwa iwe mphamvu yake: udzakhala wothawathawa ndi woyendayenda pa dziko lapansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Ukamalima mbeu, nthakayo sidzakubalira, ndipo udzakhala womangoyendayenda, wosoŵa pokhala penipeni pa dziko lapansi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Udzalima munda koma nthakayo sidzakupatsanso zokolola zake. Udzakhala wosakhazikika; womangoyendayenda pa dziko lapansi.” Onani mutuwo |