Genesis 4:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo Kaini anati kwa Yehova, Kulangidwa kwanga nkwakukulu kosapiririka. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo Kaini anati kwa Yehova, Kulangidwa kwanga nkwakukulu kosapiririka. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Kaini adauza Chauta kuti, “Chilango chimenechi nchopitirira mphamvu zanga. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Kaini anati kwa Yehova, “Chilango changa ndi chachikulu kuposera mphamvu zanga. Onani mutuwo |